Wildebeest analysis examples for: nya-nya ]
February 25, 2023 at 00:56
Script wb_pprint_html.py by Ulf Hermjakob
19356
JER 13:21
Kodi udzanena chiyani pamene
[Yehova
]
adzakuyikira anthu amene unkanena kuti ndi abale ako akukugonjetsa ndi kukulamulira? Kodi sudzamva zowawa ngati za mayi pa nthawi yake yochira?