10749 | 1CH 12:25 | Anthu a fuko la Yuda onyamula chishango ndi mkondo analipo 6,800; |
10750 | 1CH 12:26 | Anthu a fuko la Simeoni, asilikali okonzekera nkhondo analipo 7,100; |
10755 | 1CH 12:31 | Anthu a fuko la Efereimu, asilikali olimba mtima, otchuka pa mabanja awo analipo 20,800; |
10756 | 1CH 12:32 | Anthu a fuko latheka la Manase amene anawayitana kuti adzakhazikitse nawo ufumu wa Davide analipo 18,000; |
10761 | 1CH 12:37 | Anthu a fuko la Aseri, asilikali odziwa bwino nkhondo, okonzekeradi nkhondo analipo 40,000; |
11542 | 2CH 17:14 | Chiwerengero chawo potsata mabanja awo chinali chotere: kuchokera ku Yuda, atsogoleri a magulu 1,000; mtsogoleri Adina, anali ndi anthu 300,000 odziwa nkhondo; |
11543 | 2CH 17:15 | otsatana naye, mtsogoleri Yehohanani, anali ndi anthu 280,000; |
15331 | PSA 84:11 | Nʼkwabwino kukhala mʼmabwalo anu tsiku limodzi kuposa kukhala kwina kwake kwa zaka 1,000; Ine ndingakonde kukhala mlonda wa pa khomo la Nyumba ya Mulungu wanga kuposa kukhala mʼmatenti a anthu oyipa. |
20373 | JER 52:28 | Chiwerengero cha anthu amene Nebukadinezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ndi ichi: Mʼchaka cha chisanu ndi chiwiri cha ulamuliro wake, anatenga Ayuda 3,023; |
22044 | DAN 8:14 | Iye anandiyankha kuti, “Zidzachitika patapita masiku 2,300; pambuyo pake malo opatulika adzabwezeretsedwa monga kale.” |
30883 | REV 7:5 | Ochokera fuko la Yuda analipo 12,000 amene analembedwa chizindikiro. Ochokera fuko la Rubeni analipo 12,000; ochokera fuko la Gadi analipo 12,000; |
30884 | REV 7:6 | ochokera fuko la Aseri analipo 12,000; ochokera fuko la Nafutali analipo 12,000; ochokera fuko la Manase analipo 12,000; |
30885 | REV 7:7 | ochokera fuko la Simeoni analipo 12,000; ochokera fuko la Levi analipo 12,000; ochokera fuko la Isakara analipo 12,000; |
30886 | REV 7:8 | ochokera fuko la Zebuloni analipo 12,000; ochokera fuko la Yosefe analipo 12,000; ochokera fuko la Benjamini analipo 12,000. |