Wildebeest analysis examples for: nya-nya Word-Word!
February 25, 2023 at 00:56
Script wb_pprint_html.py by Ulf Hermjakob
19159
JER 6:1
“Thawani, inu anthu a ku Benjamini! Tulukani mu Yerusalemu! Lizani lipenga ku Tekowa! Kwezani mbendera ku
Beti-Hakeremu!
Pakuti tsoka lalikulu likubwera kuchokera kumpoto, ndipo chiwonongekocho nʼchachikulu.