Wildebeest analysis examples for:   nya-nya   “Word?”    February 25, 2023 at 00:56    Script wb_pprint_html.py   by Ulf Hermjakob

555  GEN 22:7  Isake anati kwa abambo ake Abrahamu, “Abambo?” Abrahamu anayankha, “Ee mwana wanga.” Isake anafunsa, “Moto ndi nkhuni zilipo, koma nanga mwana wankhosa wa nsembe yopsereza ali kuti?”