Wildebeest analysis examples for:   nya-nya   Number,Number?    February 25, 2023 at 00:56    Script wb_pprint_html.py   by Ulf Hermjakob

25653  LUK 14:31  “Kapena mfumu imene ikupita ku nkhondo kukamenyana ndi mfumu ina, kodi siyamba yakhala pansi ndi kulingalira ngati ingathe ndi anthu 10,000 kulimbana ndi amene akubwera ndi 20,000?