Wildebeest analysis examples for:   nya-nya   ASCII_DIGIT    February 11, 2023 at 19:19    Script wb_pprint_html.py   by Ulf Hermjakob

104  GEN 4:24  Ngati wopha Kaini amulipsira kasanu nʼkawiri, ndiye kuti wopha ine Lameki adzamulipsira kokwanira 77.”
109  GEN 5:3  Pamene Adamu anali ndi zaka 130, anabereka mwana wamwamuna wofanana naye ndipo anamutcha Seti.
110  GEN 5:4  Atabadwa Seti, Adamu anakhala ndi moyo zaka zina 800 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
111  GEN 5:5  Zaka zonse za Adamu zinali 930 ndipo anamwalira.
112  GEN 5:6  Pamene Seti anali ndi zaka 105, anabereka Enosi.
113  GEN 5:7  Atabadwa Enosi, Seti anakhala ndi moyo zaka zina 807 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
114  GEN 5:8  Zaka zonse za Seti zinali 912 ndipo anamwalira.
115  GEN 5:9  Pamene Enosi anali ndi zaka 90, anabereka Kenani.
116  GEN 5:10  Atabadwa Kenani, Enosi anakhala ndi moyo zaka zina 815 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
117  GEN 5:11  Zaka zonse za Enosi pamodzi zinali 905 ndipo anamwalira.
118  GEN 5:12  Pamene Kenani anali ndi zaka 70, anabereka Mahalaleli.
119  GEN 5:13  Atabadwa Mahalaleli, Kenani anakhala ndi moyo zaka zina 840 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
120  GEN 5:14  Zaka zonse za Kenani zinali 910, ndipo anamwalira.
121  GEN 5:15  Pamene Mahalaleli anali ndi zaka 65, anabereka Yaredi.
122  GEN 5:16  Atabadwa Yaredi, Mahalaleli anakhala ndi moyo zaka zina 830 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
123  GEN 5:17  Zaka zonse za Mahalaleli zinali 895 ndipo anamwalira.
124  GEN 5:18  Pamene Yaredi anali ndi zaka 162, anabereka Enoki.
125  GEN 5:19  Atabadwa Enoki, Yaredi anakhala ndi moyo zaka zina 800 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
126  GEN 5:20  Zaka zonse za Yaredi zinali 962 ndipo anamwalira.
127  GEN 5:21  Pamene Enoki anali ndi zaka 65, anabereka Metusela.
128  GEN 5:22  Atabadwa Metusela, Enoki anayenda ndi Mulungu zaka 300 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
129  GEN 5:23  Zaka zonse za Enoki zinali 365.
131  GEN 5:25  Pamene Metusela anali ndi zaka 187, anabereka Lameki.
132  GEN 5:26  Ndipo atabadwa Lameki, Metusela anakhala ndi moyo zaka zina 782 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
133  GEN 5:27  Zaka zonse za Metusela zinali 969, ndipo anamwalira.
134  GEN 5:28  Pamene Lameki anali ndi zaka 182, anabereka mwana wamwamuna.
136  GEN 5:30  Atabadwa Nowa, Lameki anakhala zaka zina 595 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
137  GEN 5:31  Zaka zonse za Lameki zinali 777, ndipo kenaka anamwalira.
138  GEN 5:32  Pamene Nowa anali ndi zaka 500, anabereka Semu, Hamu ndi Yafeti.
141  GEN 6:3  Tsono Yehova anati, “Sindilola kuti chipwirikiti chikuchitikachi chipitirire mpaka muyaya, pakuti iye ndi munthu; masiku a moyo wake adzakhala zaka 120.”
153  GEN 6:15  Uchipange motere: Chombo chikhale mamita 140 mulitali, mamita 23 mulifupi ndi mamita 13 mu msinkhu wake.
166  GEN 7:6  Pamene chigumula chinabwera pa dziko lapansi Nowa anali ndi zaka 600.
171  GEN 7:11  Pa tsiku la 17 la mwezi wachiwiri, Nowa ali ndi zaka 600, akasupe onse akuya kwambiri anasefuka ndiponso zitseko za madzi akumwamba zinatsekuka.
184  GEN 7:24  Madziwo anadzaza dziko lonse lapansi kwa masiku 150.
187  GEN 8:3  Madzi amaphwabe pa dziko lapansi. Pakutha pa masiku 150, madzi anatsika,
188  GEN 8:4  ndipo pa tsiku la 17 la mwezi wachisanu ndi chiwiri, chombo chija chinakakhazikika pa mapiri a Ararati.
197  GEN 8:13  Pofika tsiku loyamba la mwezi woyamba wa chaka chimene Nowa anakwanitsa zaka 601, madzi anawuma pa dziko lapansi. Ndipo Nowa anachotsa denga la chombo ndipo anaona kuti kunja kwawuma.
198  GEN 8:14  Pokwana tsiku la 27 la mwezi wachiwiri dziko lapansi linawumiratu.
234  GEN 9:28  Chitatha chigumula, Nowa anakhala ndi moyo zaka 350.
235  GEN 9:29  Anamwalira ali ndi zaka 950.
277  GEN 11:10  Nayi mibado yochokera kwa Semu. Patapita zaka ziwiri chitatha chigumula, Semu ali ndi zaka 100, anabereka Aripakisadi.
278  GEN 11:11  Atabereka Aripakisadi, Semu anakhala ndi moyo zaka 500 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi.
279  GEN 11:12  Pamene Aripakisadi anali ndi zaka 35, anabereka Sela.
280  GEN 11:13  Atabereka Sela, Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka zina 403 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi.
282  GEN 11:15  Atabereka Eberi, Sela anakhala ndi moyo zaka zina 403 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi.
283  GEN 11:16  Pamene Eberi anali ndi zaka 34 anabereka Pelegi.
284  GEN 11:17  Atabereka Pelegi, Eberi anakhala ndi moyo zaka zina 430 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi.
286  GEN 11:19  Atabereka Reu, Pelegi anakhala zaka zina 209 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi.
287  GEN 11:20  Pamene Reu anali ndi zaka 32, anabereka Serugi.
288  GEN 11:21  Atabereka Serugi, Reu anakhala ndi moyo zaka zina 207 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi.
290  GEN 11:23  Atabereka Nahori, Serugi anakhala ndi moyo zaka zina 200 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi.
291  GEN 11:24  Pamene Nahori anali ndi zaka 29, anabereka Tera.
292  GEN 11:25  Atabereka Tera, Nahori anakhala ndi moyo zaka zina 119 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi.
293  GEN 11:26  Pamene Tera anali ndi zaka 70, anabereka Abramu, Nahori ndi Harani.
299  GEN 11:32  Tera anamwalira ku Harani ali ndi zaka 205.
303  GEN 12:4  Choncho Abramu ananyamuka monga momwe Yehova anamuwuzira, napita pamodzi ndi Loti. Pamene Abramu amachoka ku Harani nʼkuti ali ndi zaka 75.
351  GEN 14:14  Abramu atamva kuti Loti wagwidwa pa nkhondo, anasonkhanitsa asilikali 318 obadwira mʼbanja lake lomwelo nalondola mpaka ku Dani.
374  GEN 15:13  Tsono Yehova anati kwa iye, “Uyenera kudziwa mosakayika kuti zidzukulu zako zidzakhala alendo mʼdziko lachilendo ndipo zidzakhala akapolo ndi kuzunzidwa zaka 400.
398  GEN 16:16  Pamene Hagara anamubalira Ismaeli nʼkuti Abramuyo ali ndi zaka 86.
399  GEN 17:1  Pamene Abramu anali ndi zaka 99, Yehova anamuonekera nati, “Ine ndine Mulungu Wamphamvuzonse. Ukhale munthu wochita zolungama nthawi zonse.
415  GEN 17:17  Abrahamu anadzigwetsa pansi pamaso pa Yehova, Iye anaseka nati, “Kodi munthu wa zaka 100 nʼkubala mwana? Kodi Sara adzabereka mwana pa msinkhu wa zaka makumi asanu ndi anayi?”
422  GEN 17:24  Abrahamu anali ndi zaka 99 pamene anachita mdulidwe,
453  GEN 18:28  bwanji anthu olungama atacheperapo ndi asanu pa anthu makumi asanu? Kodi mudzawononga mzinda wonse chifukwa cha asanuwo?” Iye anati, “Nditapezamo anthu 45, sindidzawuwononga.”
454  GEN 18:29  Kenakanso anayankhula kwa Iye nati, “Bwanji atangopezekamo anthu 40 okha?” Iye anayankha, “Chifukwa cha anthu 40 amenewa, sindidzatero.”
519  GEN 21:5  Abrahamu anali ndi 100 pamene mwana wake Isake anabadwa.
573  GEN 23:1  Sara anakhala ndi moyo zaka 127.
587  GEN 23:15  “Mundimvere mbuye wanga; mundawo mtengo wake ndi masekeli asiliva okwana 400. Koma zimenezo nʼchiyani pakati pa ine ndi inu? Ikani mtembo wa mkazi wanu.”
588  GEN 23:16  Abrahamu anavomera mtengo umene ananena Efroni Ahiti onse akumva ndipo anamuwerengera masekeli asiliva okwana 400 monga mwa mtengo wa ndalama umene amalonda a nthawi imeneyo ankagwiritsa ntchito.
614  GEN 24:22  Ngamira zija zitatha kumwa, mlendo uja anatulutsa chipini chagolide cholemera theka la sekeli ndi zibangiri zagolide ziwiri zolemera masekeli 100.
666  GEN 25:7  Abrahamu anakhala ndi moyo zaka 175.
676  GEN 25:17  Ismaeli anakhala ndi moyo zaka 137. Iye anamwalira ndipo anakakhala ndi anthu a mtundu wake.
685  GEN 25:26  Kenaka mʼbale wake anabadwa atagwira chidendene cha Esau; choncho anamutcha Yakobo. Isake anali ndi zaka 60 pamene Rebeka anabereka mapasawa.
727  GEN 26:34  Pamene Esau anali ndi zaka 40, anakwatira Yuditi mwana wamkazi wa Beeri Mhiti. Anakwatiranso Basemati mwana wa mkazi wa Eloni Mhiti.
935  GEN 32:7  Pamene amithenga aja anabwerera kwa Yakobo, anati, “Tinapita kwa mʼbale wanu Esau, ndipo tsopano iye akubwera kudzakumana nanu. Ali ndi anthu 400.”
943  GEN 32:15  Anasankhula mbuzi zazikazi 200 ndi atonde makumi awiri, nkhosa zazikazi 200 ndi nkhosa zazimuna makumi awiri,
944  GEN 32:16  ngamira za mkaka 30 ndi ana awo, ngʼombe zazikazi 40 ndi zazimuna khumi, ndipo abulu aakazi makumi awiri ndi abulu aamuna khumi.
962  GEN 33:1  Yakobo atakweza maso ake anaona Esau akubwera ndi anthu ake 400. Choncho ana ake anawagawira Leya, Rakele ndi antchito awiri aja.
980  GEN 33:19  Malo amenewo anagula kwa zidzukulu za Hamori, abambo a Sekemu ndi ndalama 100 zasiliva.
1040  GEN 35:28  Isake anakhala ndi moyo zaka 180.
1086  GEN 37:2  Mbiri ya banja la Yakobo ndi iyi: Yosefe, mnyamata wa zaka 17 ankaweta nkhosa ndi abale ake, pamodzi ndi ana a Biliha ndi Zilipa, akazi a abambo ake. Tsono Yosefe ankabwera kudzawuza abambo ake zoyipa za abale ake.
1242  GEN 41:46  Yosefe anali ndi zaka 30 pamene amayamba ntchito kwa Farao, mfumu ya ku Igupto. Ndipo Yosefe anachoka pa maso pa Farao nayendera dziko lonse la Igupto.
1402  GEN 46:15  Amenewa ndi ana aamuna a Leya amene anamubalira Yakobo ku Padanaramu. Panali mwana wamkazi dzina lake Dina. Ana onse analipo 33.
1405  GEN 46:18  Amenewa ndi zidzukulu za Yakobo mwa Zilipa amene Labani anapereka kwa mwana wake, Leya. Onse pamodzi analipo 16.
1413  GEN 46:26  Onse amene anapita ndi Yakobo (iwo amene anali akeake, osawerengera akazi a ana ake), analipo 66.
1414  GEN 46:27  Pophatikiza ana awiri a Yosefe obadwira ku Igupto, anthu a pa banja la Yakobo amene anapita ku Igupto, onse pamodzi analipo 70.
1430  GEN 47:9  Yakobo anayankha kuti, “Zaka za maulendo anga zakwana 130. Zaka za moyo wanga ndi zowerengeka, komanso zakhala zaka za masautso. Zaka za moyo wanga sizingafanane ndi zaka za moyo wa makolo anga.”
1449  GEN 47:28  Yakobo anakhala ku Igupto zaka 17 ndipo zaka za moyo wake zinali 147.
1510  GEN 50:3  Antchito aja zinawatengera masiku 40 kuti akonze mtembo uja popeza ntchito ngati imeneyi inafunikira masiku monga amenewa. Ndipo Aigupto anamulira Yakobo kwa masiku makumi asanu ndi awiri.
1529  GEN 50:22  Yosefe anakhala mu Igupto pamodzi ndi banja lonse la abambo ake. Anakhala ndi moyo zaka 110
1533  GEN 50:26  Choncho Yosefe anafa ali ndi zaka 110. Motero iwo atakonza thupi lake ndi mankhwala kuti lisawole, analiyika mʼbokosi ku Igupto.
1538  EXO 1:5  Anthu onse obadwa mwa Yakobo analipo 70. Yosefe nʼkuti ali kale ku Igupto.
1672  EXO 6:16  Mayina a ana a Levi pamodzi ndi zidzukulu zawo anali awa: Geresoni, Kohati ndi Merari. Levi anakhala ndi moyo kwa zaka 137.
1674  EXO 6:18  Ana a Kohati anali Amramu, Izihari, Hebroni ndi Uzieli. Kohati anakhala ndi moyo zaka 133.
1676  EXO 6:20  Amramu anakwatira Yokobedi mlongo wa abambo ake, amene anabereka Aaroni ndi Mose. Amramu anakhala ndi moyo kwa zaka 137.
1693  EXO 7:7  Mose anali ndi zaka 80, ndipo Aaroni anali ndi zaka 83 pamene anakayankhula kwa Farao.
1835  EXO 12:18  Mwezi woyamba muzidzadya buledi wopanda yisiti kuyambira madzulo tsiku la 14 la mweziwo mpaka tsiku la 21 mwezi womwewo.
1854  EXO 12:37  Aisraeli anayenda ulendo kuchokera ku Ramesesi mpaka kukafika ku Sukoti. Anthu aamuna oyenda pansi analipo 600,000 osawerengera akazi ndi ana.
1857  EXO 12:40  Ndipo Aisraeli anakhala ku Igupto kwa zaka 430.
1858  EXO 12:41  Pa tsiku lomwelo limene anakwanitsa zaka 430, magulu onse a Yehova anatuluka mʼdziko la Igupto.
1897  EXO 14:7  Iye anatenga magaleta 600 abwino kwambiri pamodzi ndi magaleta ena a dziko la Igupto. Anatenganso akuluakulu onse ankhondo.
1983  EXO 16:35  Aisraeli anadya mana zaka 40, mpaka pamene anafika ku dziko kumene amati akakhazikeko. Iwo anadya mana mpaka pamene anafika mʼmalire a Kanaani.
2021  EXO 18:21  Koma sankhani amuna odziwa ntchito yawo, anthu owopa Mulungu, anthu odalirika amene amadana ndi kupeza phindu mwachinyengo. Tsono muwayike kuti akhale oyangʼanira anthu motere: atsogoleri a anthu 1,000, ena a anthu 100, ena a anthu 50 ndi ena a anthu khumi.
2025  EXO 18:25  Iye anasankha amuna odziwa bwino ntchito zawo ndipo anawayika kuti akhale atsogoleri, oyangʼanira anthu motere: atsogoleri a anthu 1,000, ena a anthu 500, ena a anthu makumi asanu ndi ena a anthu khumi.
2196  EXO 24:18  Ndipo Mose analowa mʼmitambo nakwera phiri. Iye anakhala ku phiriko 40 usana ndi usiku.
2206  EXO 25:10  “Tsono apange bokosi lamatabwa amtengo wa mkesha, ndipo kutalika kwake kukhale masentimita 114, mulifupi mwake masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69.
2213  EXO 25:17  “Upange chivundikiro cha bokosilo cha golide wabwino kwambiri, kutalika kwake masentimita 114, mulifupi mwake masentimita 69.
2219  EXO 25:23  “Upange tebulo la matabwa amtengo wa mkesha, mulitali mwake masentimita 91, mulifupi mwake masentimita 46, msinkhu wake masentimita 69.
2235  EXO 25:39  Choyikapo nyale ndi zipangizo zonse zipangidwe ndi golide wabwino kwambiri wolemera makilogalamu 34.
2241  EXO 26:5  Upange zokolowekamo 50 pa nsalu yoyamba ndi zokolowekamo makumi asanu zinanso pa nsalu inayo. Upange motero kuti zokolowekamozo ziziyangʼanana.
2246  EXO 26:10  Upange zokolowekamo 50 mʼmphepete mwa nsalu imodzi yotsirizira ya nsalu yoyamba yolumikiza ija. Upangenso zokolowekamo zina 50 mʼmphepete mwa nsalu yotsirizira ya nsalu inanso yolumikiza ija.
2247  EXO 26:11  Kenaka upange ngowe 50 zamkuwa ndipo uzilowetse mu zokolowekazo. Ndiye uphatikize nsalu ziwirizo kuti tentiyo ikhale imodzi.
2249  EXO 26:13  Nsalu yotsalira ya masentimita 46 mulitali mwake mʼmbali zonse ziwiri idzalendewere kuphimba mbali ziwirizo.
2252  EXO 26:16  Feremu iliyonse ikhale yotalika mamita anayi ndipo mulifupi mwake mukhale masentimita 69.
2255  EXO 26:19  Ndipo upange matsinde 40 asiliva ndipo uwayike pansi pa maferemuwo. Pansi pa feremu iliyonse pakhale matsinde awiri ogwiriziza zolumikizira ziwiri zija.
2257  EXO 26:21  Upangenso matsinde 40 asiliva, awiri pansi pa feremu iliyonse.
2261  EXO 26:25  Choncho pakhale maferemu asanu ndi atatu ndiponso matsinde 16 asiliva, awiri akhale pansi pa feremu iliyonse.
2274  EXO 27:1  “Upange guwa lansembe lamatabwa amtengo wa mkesha. Likhale lofanana mbali zonse, msinkhu wake masentimita 137, mulitali mwake masentimita 229, mulifupi mwake masentimita 229.
2282  EXO 27:9  “Upange bwalo la chihema. Mbali yakummwera ikhale yotalika mamita 46 ndipo ikhale ndi nsalu yotchinga yofewa yosalala yolukidwa bwino.
2284  EXO 27:11  Mbali yakumpoto ikhalenso yotalika mamita 46 ndipo ikhale ndi nsalu yotchinga. Pakhalenso mizati makumi awiri, matsinde amkuwa makumi awiri, ngowe zasiliva ndi zingwe za mizatiyo.
2285  EXO 27:12  “Mbali yakumadzulo ya bwalolo ikhale yotalika mamita 23 ndipo ikhale ndi nsalu yotchinga, nsichi khumi ndi matsinde khumi.
2286  EXO 27:13  Mbali yakummawa, kotulukira dzuwa, kutalika kwa bwalo kukhale mamita 23.
2291  EXO 27:18  Kutalika kwa bwalolo kukhale mamita 46, mulifupi mwake mamita 23, msinkhu wake masentimita 230. Nsalu ya katani ikhale yofewa ndi yosalala bwino. Matsinde ake akhale amkuwa.
2310  EXO 28:16  Kutalika kwake kukhale kofanana mbali zonse, mulitali masentimita 23, mulifupi masentimita 23, ndipo chikhale chopinda pawiri.
2385  EXO 30:2  Likhale lofanana mbali zonse. Mulitali masentimita 46, mulifupi masentimita 46, ndipo msinkhu masentimita 91. Nyanga zake zipangidwe kumodzi ndi guwalo.
2467  EXO 32:28  Alevi anachita zomwe Mose analamula, ndipo tsiku limenelo panafa anthu pafupifupi 3,000.
2525  EXO 34:28  Mose anakhala kumeneko pamodzi ndi Yehova masiku 40, usana ndi usiku, wosadya kanthu kapena kumwa madzi. Ndipo iye analemba pa miyala ija mawu a pangano, malamulo khumi.
2580  EXO 36:13  Kenaka anapanga ngowe zagolide 50 zolumikizira nsalu ziwirizo kotero kuti zinapanga chihema chimodzi.
2585  EXO 36:18  Iwo anapanga ngowe 50 zamkuwa zolowetsa mu zokolowekazo ndipo anaphatikiza nsalu ziwirizo kuti tentiyo ikhale imodzi.
2588  EXO 36:21  Feremu iliyonse inali yotalika mamita anayi ndipo mulifupi mwake munali masentimita 69.
2591  EXO 36:24  ndiponso anapanga matsinde 40 asiliva ndipo anawayika pansi pa maferemuwo. Pansi pa feremu iliyonse anayika matsinde awiri ogwiriziza zolumikizira ziwiri zija.
2597  EXO 36:30  Choncho panali maferemu asanu ndi atatu ndiponso matsinde 16 asiliva, awiri anali pansi pa feremu iliyonse.
2606  EXO 37:1  Bezaleli anapanga Bokosi la Chipangano lamatabwa amtengo wa mkesha. Kutalika kwake kunali masentimita 114, mulifupi mwake munali masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69.
2611  EXO 37:6  Iye anapanga chivundikiro cha bokosilo cha golide wabwino kwambiri, kutalika kwake masentimita 114, mulifupi mwake masentimita 69.
2615  EXO 37:10  Iwo anapanga tebulo la matabwa amtengo wa mkesha, mulitali mwake masentimita 91, mulifupi mwake masentimita 46, msinkhu wake masentimita 69.
2629  EXO 37:24  Iwo anapanga choyikapo nyale ndi zipangizo zake zonse zagolide wabwino kwambiri wolemera makilogalamu 34.
2630  EXO 37:25  Iwo anapanga guwa lamatabwa amtengo wa mkesha lofukizirapo lubani. Linali lofanana mbali zonse, mulitali masentimita 46, mulifupi masentimita 46, ndipo msinkhu masentimita 91, ndipo nyanga zake zinapangidwa kumodzi ndi guwalo.
2635  EXO 38:1  Anapanga guwa lansembe zopsereza lamatabwa amtengo wa mkesha. Linali lofanana mbali zonse. Msinkhu wake masentimita 137, mulitali mwake masentimita 229, mulifupi masentimita 229.
2643  EXO 38:9  Kenaka anapanga bwalo la chihema. Mbali yakummwera inali yotalika mamita 46 ndipo kunali nsalu yotchinga yofewa yosalala yolukidwa bwino.
2645  EXO 38:11  Mbali yakumpoto inalinso yotalika mamita 46 ndipo inali ndi mizati makumi awiri, matsinde amkuwa makumi awiri, ngowe zasiliva ndi zingwe za mizatiyo.
2646  EXO 38:12  Mbali yakumadzulo inali yotalika mamita 23 ndipo inali ndi nsalu yotchinga, mizati khumi ndi matsinde khumi. Inalinso ndi ngowe zasiliva ndi zingwe za mizatiyo.
2647  EXO 38:13  Mbali yakummawa, kotulukira dzuwa, inalinso yotalika mamita 23.
2652  EXO 38:18  Nsalu yotchinga ya pa chipata inali yamtundu wa mtambo, yapepo ndi yofiira, yofewa yosalala ndi yopangidwa ndi anthu aluso. Nsaluyo inali yotalika mamita asanu ndi anayi, molingana ndi nsalu zotchinga bwalo. Msinkhu wake unali masentimita 229,
2658  EXO 38:24  Golide yense wochokera ku nsembe yoweyula amene anagwiritsa ntchito pa ntchito yonse yopanga malo wopatulika anali wolemera makilogalamu 1,000 potsata miyeso ya kumalo wopatulika.
2659  EXO 38:25  Siliva wochokera ku gulu lonse la anthu anali wolemerera makilogalamu 3,430, potsata miyeso ya ku malo wopatulika.
2660  EXO 38:26  Munthu aliyense amapereka beka imodzi, kufanana ngati makilogalamu 6, potsata muyeso wa ku malo wopatulika. Kuchokera kwa aliyense amene anawerengedwa kuyambira zaka 20 kapena kuposerapo, amuna onse analipo 603,550.
2661  EXO 38:27  Anagwiritsa ntchito siliva wolemera makilogalamu 3,400 kupanga matsinde 100 a ku malo wopatulika ndi makatani, ndipo makilogalamu 34 kupanga tsinde limodzi.
2663  EXO 38:29  Mkuwa ochokera ku nsembe yoweyula unali makilogalamu 2,425.
2674  EXO 39:9  Kutalika kwake kunali kofanana mbali zonse, mulitali masentimita 23, mulifupi masentimita 23, chinali chopinda pawiri.
2747  LEV 1:1  26 Yehova anayitana Mose mu tenti ya msonkhano. Iye anati,
3049  LEV 12:4  Mkaziyo adikire masiku ena 33 kuti ayeretsedwe ku matenda ake. Asakhudze kanthu kalikonse koyera kapena kulowa mʼmalo wopatulika mpaka masiku a kuyeretsedwa kwake atatha.
3050  LEV 12:5  Ngati abala mwana wamkazi, adzakhala wodetsedwa kwa masabata awiri, monga zikhalira pa nthawi yake yosamba. Ndipo mkaziyo adikire masiku ena 66, kuti ayeretsedwe ku matenda akewo.
3408  LEV 23:5  Chikondwerero cha Paska chiziyamba madzulo a tsiku la 14 la mwezi woyamba.
3409  LEV 23:6  Tsiku la 15 la mwezi womwewo ndi tsiku lolemekeza Yehova ndipo muziyamba Chikondwerero cha Buledi Wopanda Yisiti. Muzidya buledi wopanda yisiti kwa masiku asanu ndi awiri.
3437  LEV 23:34  “Uwawuze Aisraeli kuti pa masiku asanu ndi awiri kuyambira pa tsiku la 15 la mwezi wachisanu ndi chiwiri pazikhala Chikondwerero cha Misasa cholemekeza Yehova.
3442  LEV 23:39  “ ‘Choncho kuyambira pa tsiku la 15 la mwezi wachisanu ndi chiwiri, mutakolola zinthu mʼmunda mwanu, muchite chikondwerero cha Yehova kwa masiku asanu ndi awiri. Tsiku loyamba ndi tsiku lopumula, ndipo tsiku lachisanu ndi chitatu ndi lopumulanso.
3478  LEV 25:8  “ ‘Muzichotsera Masabata asanu ndi awiri a zaka, ndi kuchulukitsa zaka zisanu ndi ziwiri kasanu ndi kawirinso kuti Masabata asanu ndi awiri a zakawo akwane zaka 49.
3533  LEV 26:8  Anthu asanu mwa inu adzapirikitsa anthu 100, ndipo anthu 100 mwa inu adzathamangitsa anthu 10,000, ndipo adani anuwo mudzawagonjetsa ndi lupanga.
3574  LEV 27:3  mtengo wake ukhale masekeli a siliva makumi asanu, molingana ndi kawerengedwe ka ku Nyumba ya Mulungu, ngati munthuyo ndi wamwamuna wa zaka zapakati pa 20 ndi 60.
3626  NUM 1:21  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Rubeni chinali 46,500.
3628  NUM 1:23  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Simeoni chinali 59,300.
3630  NUM 1:25  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Gadi chinali 45, 650.
3632  NUM 1:27  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Yuda chinali 74, 600.
3634  NUM 1:29  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Isakara chinali 54,400.
3636  NUM 1:31  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Zebuloni chinali 57,400.
3638  NUM 1:33  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Efereimu chinali 40,500.
3640  NUM 1:35  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Manase chinali 32,200.
3642  NUM 1:37  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Benjamini chinali 35,400.
3644  NUM 1:39  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Dani chinali 62,700.
3646  NUM 1:41  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Aseri chinali 41,500.
3648  NUM 1:43  Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Nafutali chinali 53,400.
3651  NUM 1:46  Chiwerengero cha anthu onse pamodzi chinali 603,550.
3663  NUM 2:4  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 74,600.
3665  NUM 2:6  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 54,400.
3667  NUM 2:8  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 57,400.
3668  NUM 2:9  Anthu onse aamuna mʼmisasa ya Yuda, chiwerengero chawo ndi 186,400 monga mwa magulu awo. Iwowo ndiwo aziyamba kusamuka.
3670  NUM 2:11  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 46,500.
3672  NUM 2:13  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 59,300.
3674  NUM 2:15  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 45,650.
3675  NUM 2:16  Anthu onse aamuna mu msasa wa Rubeni, chiwerengero chawo monga mwa magulu awo, ndi 151,450. Iwowo azikhala achiwiri posamuka.
3678  NUM 2:19  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 40,500.
3680  NUM 2:21  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 32,200.
3682  NUM 2:23  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 35,400.
3683  NUM 2:24  Anthu onse aamuna mu msasa wa Efereimu, chiwerengero chawo ndi 108,100 monga mwa magulu awo. Iwowo azikhala achitatu posamuka.
3685  NUM 2:26  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 62,700.
3687  NUM 2:28  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 41,500.
3689  NUM 2:30  Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 53,400.
3690  NUM 2:31  Anthu onse aamuna mu msasa wa Dani chiwerengero chawo ndi 157,600. Iwo azidzanyamuka pomaliza, ndi mbendera zawo.
3691  NUM 2:32  Amenewa ndi Aisraeli monga mwa mabanja a makolo awo. Chiwerengero cha Aisraeli onse mʼmisasa chinali 603,550, mwa magulu awo.
3715  NUM 3:22  Chiwerengero cha amuna onse amene anawawerenga a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 7,500.
3721  NUM 3:28  Chiwerengero cha amuna onse a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 8,600. Akohati ankagwira ntchito yosamalira malo wopatulika.
3727  NUM 3:34  Chiwerengero cha amuna onse kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 6,200.
3732  NUM 3:39  Alevi onse amene Mose ndi Aaroni anawawerenga potsatira lamulo la Yehova monga mwa magulu a mabanja awo, amuna onse kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo anali 22,000.
3736  NUM 3:43  Chiwerengero chonse cha ana aamuna oyamba kubadwa kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 22, 273.
3739  NUM 3:46  Pofuna kuwombola ana aamuna 273 oyamba kubadwa a Aisraeli amene anaposa chiwerengero cha aamuna a fuko la Levi,
3743  NUM 3:50  Anatenga masekeli a siliva okwana 1,365 molingana ndi masekeli a ku malo opatulika, kuchokera kwa ana aamuna oyamba kubadwa a Aisraeli.
3780  NUM 4:36  atawawerenga mwa mafuko awo, anali 2,750.
3784  NUM 4:40  atawawerenga mwa mafuko ndi mabanja awo, anali 2,630.
3788  NUM 4:44  atawawerenga mwa mafuko ndi mabanja awo, anali 3,200.
3792  NUM 4:48  analipo 8,580.
3864  NUM 7:13  Chopereka chake chinali mbale imodzi yasiliva yolemera kilogalamu imodzi, ndi beseni lasiliva limodzi lowazira, lolemera magalamu 800, zonse monga mwa muyeso wa ku malo wopatulika ndipo zonse ziwiri zinali zodzaza ndi ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta ngati chopereka chachakudya;