Wildebeest analysis examples for:   nya-nya   ]    February 11, 2023 at 19:19    Script wb_pprint_html.py   by Ulf Hermjakob

19356  JER 13:21  Kodi udzanena chiyani pamene [Yehova] adzakuyikira anthu amene unkanena kuti ndi abale ako akukugonjetsa ndi kukulamulira? Kodi sudzamva zowawa ngati za mayi pa nthawi yake yochira?