112 | GEN 5:6 | Pamene Seti anali ndi zaka 105, anabereka Enosi. |
116 | GEN 5:10 | Atabadwa Kenani, Enosi anakhala ndi moyo zaka zina 815 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. |
117 | GEN 5:11 | Zaka zonse za Enosi pamodzi zinali 905 ndipo anamwalira. |
121 | GEN 5:15 | Pamene Mahalaleli anali ndi zaka 65, anabereka Yaredi. |
123 | GEN 5:17 | Zaka zonse za Mahalaleli zinali 895 ndipo anamwalira. |
127 | GEN 5:21 | Pamene Enoki anali ndi zaka 65, anabereka Metusela. |
129 | GEN 5:23 | Zaka zonse za Enoki zinali 365. |
136 | GEN 5:30 | Atabadwa Nowa, Lameki anakhala zaka zina 595 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. |
138 | GEN 5:32 | Pamene Nowa anali ndi zaka 500, anabereka Semu, Hamu ndi Yafeti. |
184 | GEN 7:24 | Madziwo anadzaza dziko lonse lapansi kwa masiku 150. |
187 | GEN 8:3 | Madzi amaphwabe pa dziko lapansi. Pakutha pa masiku 150, madzi anatsika, |
234 | GEN 9:28 | Chitatha chigumula, Nowa anakhala ndi moyo zaka 350. |
235 | GEN 9:29 | Anamwalira ali ndi zaka 950. |
278 | GEN 11:11 | Atabereka Aripakisadi, Semu anakhala ndi moyo zaka 500 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi. |
279 | GEN 11:12 | Pamene Aripakisadi anali ndi zaka 35, anabereka Sela. |
299 | GEN 11:32 | Tera anamwalira ku Harani ali ndi zaka 205. |
303 | GEN 12:4 | Choncho Abramu ananyamuka monga momwe Yehova anamuwuzira, napita pamodzi ndi Loti. Pamene Abramu amachoka ku Harani nʼkuti ali ndi zaka 75. |
453 | GEN 18:28 | bwanji anthu olungama atacheperapo ndi asanu pa anthu makumi asanu? Kodi mudzawononga mzinda wonse chifukwa cha asanuwo?” Iye anati, “Nditapezamo anthu 45, sindidzawuwononga.” |
666 | GEN 25:7 | Abrahamu anakhala ndi moyo zaka 175. |
2021 | EXO 18:21 | Koma sankhani amuna odziwa ntchito yawo, anthu owopa Mulungu, anthu odalirika amene amadana ndi kupeza phindu mwachinyengo. Tsono muwayike kuti akhale oyangʼanira anthu motere: atsogoleri a anthu 1,000, ena a anthu 100, ena a anthu 50 ndi ena a anthu khumi. |
2025 | EXO 18:25 | Iye anasankha amuna odziwa bwino ntchito zawo ndipo anawayika kuti akhale atsogoleri, oyangʼanira anthu motere: atsogoleri a anthu 1,000, ena a anthu 500, ena a anthu makumi asanu ndi ena a anthu khumi. |
2241 | EXO 26:5 | Upange zokolowekamo 50 pa nsalu yoyamba ndi zokolowekamo makumi asanu zinanso pa nsalu inayo. Upange motero kuti zokolowekamozo ziziyangʼanana. |
2246 | EXO 26:10 | Upange zokolowekamo 50 mʼmphepete mwa nsalu imodzi yotsirizira ya nsalu yoyamba yolumikiza ija. Upangenso zokolowekamo zina 50 mʼmphepete mwa nsalu yotsirizira ya nsalu inanso yolumikiza ija. |
2247 | EXO 26:11 | Kenaka upange ngowe 50 zamkuwa ndipo uzilowetse mu zokolowekazo. Ndiye uphatikize nsalu ziwirizo kuti tentiyo ikhale imodzi. |
2580 | EXO 36:13 | Kenaka anapanga ngowe zagolide 50 zolumikizira nsalu ziwirizo kotero kuti zinapanga chihema chimodzi. |
2585 | EXO 36:18 | Iwo anapanga ngowe 50 zamkuwa zolowetsa mu zokolowekazo ndipo anaphatikiza nsalu ziwirizo kuti tentiyo ikhale imodzi. |
2660 | EXO 38:26 | Munthu aliyense amapereka beka imodzi, kufanana ngati makilogalamu 6, potsata muyeso wa ku malo wopatulika. Kuchokera kwa aliyense amene anawerengedwa kuyambira zaka 20 kapena kuposerapo, amuna onse analipo 603,550. |
2663 | EXO 38:29 | Mkuwa ochokera ku nsembe yoweyula unali makilogalamu 2,425. |
3409 | LEV 23:6 | Tsiku la 15 la mwezi womwewo ndi tsiku lolemekeza Yehova ndipo muziyamba Chikondwerero cha Buledi Wopanda Yisiti. Muzidya buledi wopanda yisiti kwa masiku asanu ndi awiri. |
3437 | LEV 23:34 | “Uwawuze Aisraeli kuti pa masiku asanu ndi awiri kuyambira pa tsiku la 15 la mwezi wachisanu ndi chiwiri pazikhala Chikondwerero cha Misasa cholemekeza Yehova. |
3442 | LEV 23:39 | “ ‘Choncho kuyambira pa tsiku la 15 la mwezi wachisanu ndi chiwiri, mutakolola zinthu mʼmunda mwanu, muchite chikondwerero cha Yehova kwa masiku asanu ndi awiri. Tsiku loyamba ndi tsiku lopumula, ndipo tsiku lachisanu ndi chitatu ndi lopumulanso. |
3626 | NUM 1:21 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Rubeni chinali 46,500. |
3628 | NUM 1:23 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Simeoni chinali 59,300. |
3630 | NUM 1:25 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Gadi chinali 45, 650. |
3634 | NUM 1:29 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Isakara chinali 54,400. |
3636 | NUM 1:31 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Zebuloni chinali 57,400. |
3638 | NUM 1:33 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Efereimu chinali 40,500. |
3642 | NUM 1:37 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Benjamini chinali 35,400. |
3646 | NUM 1:41 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Aseri chinali 41,500. |
3648 | NUM 1:43 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Nafutali chinali 53,400. |
3651 | NUM 1:46 | Chiwerengero cha anthu onse pamodzi chinali 603,550. |
3665 | NUM 2:6 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 54,400. |
3667 | NUM 2:8 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 57,400. |
3670 | NUM 2:11 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 46,500. |
3672 | NUM 2:13 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 59,300. |
3674 | NUM 2:15 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 45,650. |
3675 | NUM 2:16 | Anthu onse aamuna mu msasa wa Rubeni, chiwerengero chawo monga mwa magulu awo, ndi 151,450. Iwowo azikhala achiwiri posamuka. |
3678 | NUM 2:19 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 40,500. |
3682 | NUM 2:23 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 35,400. |
3687 | NUM 2:28 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 41,500. |
3689 | NUM 2:30 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 53,400. |
3690 | NUM 2:31 | Anthu onse aamuna mu msasa wa Dani chiwerengero chawo ndi 157,600. Iwo azidzanyamuka pomaliza, ndi mbendera zawo. |
3691 | NUM 2:32 | Amenewa ndi Aisraeli monga mwa mabanja a makolo awo. Chiwerengero cha Aisraeli onse mʼmisasa chinali 603,550, mwa magulu awo. |
3715 | NUM 3:22 | Chiwerengero cha amuna onse amene anawawerenga a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 7,500. |
3743 | NUM 3:50 | Anatenga masekeli a siliva okwana 1,365 molingana ndi masekeli a ku malo opatulika, kuchokera kwa ana aamuna oyamba kubadwa a Aisraeli. |
3780 | NUM 4:36 | atawawerenga mwa mafuko awo, anali 2,750. |
3792 | NUM 4:48 | analipo 8,580. |
4197 | NUM 16:2 | ndipo anawukira Mose. Mʼgulu mwawo munali atsogoleri a Aisraeli 250, anthu otchuka amene anasankhidwa ndi anthu pa msonkhano. |
4212 | NUM 16:17 | Munthu aliyense akatenge chofukizira ndi kuyikamo lubani, zofukizira 250 zonse pamodzi ndi kuzibweretsa pamaso pa Yehova. Iwe ndi Aaroni mudzabweretsenso zofukizira zanu.” |
4230 | NUM 16:35 | Ndipo moto wochokera kwa Yehova unabwera nʼkunyeketsa anthu 250 amene ankapereka nsembe yofukiza aja. |
4501 | NUM 26:10 | Nthaka inangʼambika ndi kuwameza pamodzi ndi Kora, kotero kuti gulu lawo linafa pamene moto unapsereza anthu 250 aja, nasanduka chenjezo. |
4509 | NUM 26:18 | Awa ndiwo anali mafuko a Gadi. Onse amene anawerengedwa analipo 40,500. |
4513 | NUM 26:22 | Awa ndiwo anali mafuko a Yuda. Amene anawerenga analipo 76,500. |
4518 | NUM 26:27 | Awa ndiwo anali mafuko a Zebuloni. Amene anawerengedwa analipo 60,500. |
4525 | NUM 26:34 | Awa ndiwo anali mafuko a Manase. Amene anawerengedwa analipo 52,700. |
4528 | NUM 26:37 | Awa ndiwo anali mafuko a Efereimu. Amene anawerengedwa analipo 32,500. Zimenezi zinali zidzukulu za Yosefe monga mwa mafuko awo. |
4532 | NUM 26:41 | Awa ndiwo anali mabanja a Benjamini. Amene nawerengedwa analipo 45,600. |
4538 | NUM 26:47 | Awa ndiwo anali mafuko a Aseri. Onse amene anawerengedwa analipo 53,400. |
4541 | NUM 26:50 | Awa ndiwo anali mafuko a Nafutali. Onse amene anawerengedwa analipo 45,400. |
4596 | NUM 28:17 | Pa tsiku la 15 la mwezi womwewo pazikhala chikondwerero. Muzidya buledi wopanda yisiti kwa masiku asanu ndi awiri. |
4694 | NUM 31:28 | Pa gawo la ankhondowo, mutengeko gawo la Yehova, pa zofunkha 500 zilizonse mutengeko chimodzi, pa akapolo, ngʼombe, bulu ndi nkhosa. |
4698 | NUM 31:32 | Zotsala pa zolanda ku nkhondo zimene ankhondowo anatenga zinali nkhosa 675,000, |
4702 | NUM 31:36 | Gawo la ankhondo amene anapita ku nkhondo linali: nkhosa 337,500, |
4703 | NUM 31:37 | mwa zimenezi gawo la Yehova linali 675; |
4705 | NUM 31:39 | abulu analipo 30,500 ndipo gawo la Yehova linali 61; |
4709 | NUM 31:43 | Tsono gawo la Aisraeli linali ili: nkhosa 337,500, |
4711 | NUM 31:45 | abulu 30,500, |
4765 | NUM 33:3 | Aisraeli ananyamuka kuchokera ku Ramesesi pa tsiku la 15 la mwezi woyamba, itangotha Paska. Iwo anatuluka nayenda molimba mtima Aigupto onse akuona, |
4851 | NUM 35:4 | “Malo a msipu a mudziwo amene mudzawapatse Aleviwo, adzayambire ku khoma la mudzi ndipo adzatuluke kunja mamita 450, kuzungulira mudziwo. |
6016 | JOS 8:12 | Yoswa anali atatenga asilikali 5,000 ndi kuwabisa pakati pa Ai ndi Beteli, kumadzulo kwa mzindawo. |
6199 | JOS 14:10 | “Tsono papita zaka 45 chiyankhulire Yehova zimenezi kwa Mose. Nthawi imeneyo nʼkuti Aisraeli akuyendayenda mʼchipululu. Yehova wandisunga ndipo tsopano ndili ndi zaka 85. |
6731 | JDG 8:10 | Nthawi iyi nʼkuti Zeba ndi Zalimuna ali ku Karikori ndi ankhondo pafupifupi 15,000. Amenewa ndiwo anatsalako mwa ankhondo a anthu akummawa; pakuti anafa ankhondo 120,000. |
7091 | JDG 20:35 | Tsono Yehova anagonjetsa Abenjamini pamaso pa Israeli motero kuti Aisraeli anapha ankhondo a Abenjamini 25,100 tsiku limenelo. |
7101 | JDG 20:45 | Koma ena anatembenuka nathawira ku chipululu ku thanthwe la Rimoni. Mwa iwowa Aisraeli anapha Abenjamini 5,000 mʼmisewu yayikulu. Anawapitikitsabe Abenjaminiwo mpaka kufika ku Gidomu ndi kuphanso ena 2,000. |
7102 | JDG 20:46 | Pa tsiku limenelo Abenjamini olimba mtima okhala ndi malupanga okwana 25,000 anafa. |
7625 | 1SA 17:5 | Iye ankavala chipewa chamkuwa ndi malaya achitsulo olemera makilogalamu 57. |
7808 | 1SA 22:18 | Kotero mfumu inalamula Doegi kuti, “Uwaphe ndiwe ansembewa.” Choncho Doegi Mwedomu anapita ndi kuwapha. Tsiku limenelo iye anapha amuna 85 amene amavala efodi wa nsalu yofewa. |
8704 | 2SA 24:9 | Yowabu anapereka chiwerengero cha anthu ankhondo kwa mfumu: Mu Israeli munali anthu 800,000 amphamvu amene amadziwa kugwiritsa ntchito lupanga ndipo mu Yuda munali anthu 500,000. |
8725 | 1KI 1:5 | Nthawi imeneyi Adoniya, mwana wa Hagiti, anayamba kudzitukumula ndipo anati, “Ndidzakhala mfumu ndine.” Choncho anadzikonzera galeta ndi akavalo, pamodzi ndi anthu 50 woti azithamanga patsogolo pake. |
8869 | 1KI 5:2 | Chakudya cha tsiku ndi tsiku cha Solomoni chinali madengu 150 a ufa wosalala ndi madengu 300 a mgayiwa, |
8879 | 1KI 5:12 | Solomoni anapeka miyambi 3,000 ndi kulemba nyimbo 1,005. |
8940 | 1KI 7:3 | Pamwamba pa mitandapo panali matabwa a mkungudza amene anaphimba zipinda zimene zinamangidwa pa nsanamira 45, pa mzere uliwonse nsanamira 15. |
9077 | 1KI 9:23 | Amenewa ndiwo anali akuluakulu oyangʼanira ntchito za Solomoni. Anthu okwana 550 ndiwo ankayangʼanira anthu amene ankagwira ntchitowo. |
9111 | 1KI 10:29 | Ankagula magaleta ku Igupto pa mtengo wa masekeli asiliva okwana 600, ndipo akavalo pa mtengo wa masekeli 150. Anthu amalondawo ankagulitsa zimenezi kwa mafumu onse a Ahiti ndi Asiriya. |
9186 | 1KI 12:32 | Iye anakhazikitsa chikondwerero pa tsiku la 15 la mwezi wachisanu ndi chitatu, lofanana ndi tsiku la chikondwerero cha ku Yuda, ndipo ankapereka nsembe pa guwa. Izi ankachita ku Beteli, kupereka nsembe kwa ana angʼombe amene anapanga. Ndipo ku Beteliko anayikako ansembe pa malo achipembedzo amene anamanga. |