2467 | EXO 32:28 | Alevi anachita zomwe Mose analamula, ndipo tsiku limenelo panafa anthu pafupifupi 3,000. |
2660 | EXO 38:26 | Munthu aliyense amapereka beka imodzi, kufanana ngati makilogalamu 6, potsata muyeso wa ku malo wopatulika. Kuchokera kwa aliyense amene anawerengedwa kuyambira zaka 20 kapena kuposerapo, amuna onse analipo 603,550. |
2663 | EXO 38:29 | Mkuwa ochokera ku nsembe yoweyula unali makilogalamu 2,425. |
3626 | NUM 1:21 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Rubeni chinali 46,500. |
3628 | NUM 1:23 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Simeoni chinali 59,300. |
3634 | NUM 1:29 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Isakara chinali 54,400. |
3636 | NUM 1:31 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Zebuloni chinali 57,400. |
3638 | NUM 1:33 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Efereimu chinali 40,500. |
3640 | NUM 1:35 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Manase chinali 32,200. |
3642 | NUM 1:37 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Benjamini chinali 35,400. |
3644 | NUM 1:39 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Dani chinali 62,700. |
3646 | NUM 1:41 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Aseri chinali 41,500. |
3648 | NUM 1:43 | Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Nafutali chinali 53,400. |
3651 | NUM 1:46 | Chiwerengero cha anthu onse pamodzi chinali 603,550. |
3663 | NUM 2:4 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 74,600. |
3665 | NUM 2:6 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 54,400. |
3667 | NUM 2:8 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 57,400. |
3670 | NUM 2:11 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 46,500. |
3672 | NUM 2:13 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 59,300. |
3674 | NUM 2:15 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 45,650. |
3675 | NUM 2:16 | Anthu onse aamuna mu msasa wa Rubeni, chiwerengero chawo monga mwa magulu awo, ndi 151,450. Iwowo azikhala achiwiri posamuka. |
3678 | NUM 2:19 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 40,500. |
3680 | NUM 2:21 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 32,200. |
3682 | NUM 2:23 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 35,400. |
3685 | NUM 2:26 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 62,700. |
3687 | NUM 2:28 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 41,500. |
3689 | NUM 2:30 | Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 53,400. |
3690 | NUM 2:31 | Anthu onse aamuna mu msasa wa Dani chiwerengero chawo ndi 157,600. Iwo azidzanyamuka pomaliza, ndi mbendera zawo. |
3715 | NUM 3:22 | Chiwerengero cha amuna onse amene anawawerenga a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 7,500. |
3721 | NUM 3:28 | Chiwerengero cha amuna onse a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 8,600. Akohati ankagwira ntchito yosamalira malo wopatulika. |
3727 | NUM 3:34 | Chiwerengero cha amuna onse kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 6,200. |
3732 | NUM 3:39 | Alevi onse amene Mose ndi Aaroni anawawerenga potsatira lamulo la Yehova monga mwa magulu a mabanja awo, amuna onse kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo anali 22,000. |
3780 | NUM 4:36 | atawawerenga mwa mafuko awo, anali 2,750. |
3784 | NUM 4:40 | atawawerenga mwa mafuko ndi mabanja awo, anali 2,630. |
3788 | NUM 4:44 | atawawerenga mwa mafuko ndi mabanja awo, anali 3,200. |
3792 | NUM 4:48 | analipo 8,580. |
4498 | NUM 26:7 | Awa anali mafuko a Rubeni: onse amene anawerengedwa analipo 43,730. |
4505 | NUM 26:14 | Awa anali mafuko a Simeoni. Iwowa analipo amuna 22,200. |
4509 | NUM 26:18 | Awa ndiwo anali mafuko a Gadi. Onse amene anawerengedwa analipo 40,500. |
4513 | NUM 26:22 | Awa ndiwo anali mafuko a Yuda. Amene anawerenga analipo 76,500. |
4516 | NUM 26:25 | Awa ndi amene anali a fuko la Isakara. Amene anawerengedwa analipo 64,300. |
4518 | NUM 26:27 | Awa ndiwo anali mafuko a Zebuloni. Amene anawerengedwa analipo 60,500. |
4525 | NUM 26:34 | Awa ndiwo anali mafuko a Manase. Amene anawerengedwa analipo 52,700. |
4528 | NUM 26:37 | Awa ndiwo anali mafuko a Efereimu. Amene anawerengedwa analipo 32,500. Zimenezi zinali zidzukulu za Yosefe monga mwa mafuko awo. |
4532 | NUM 26:41 | Awa ndiwo anali mabanja a Benjamini. Amene nawerengedwa analipo 45,600. |
4534 | NUM 26:43 | Onse a fuko la Asuhamu amene anawerengedwa analipo 64,400. |
4538 | NUM 26:47 | Awa ndiwo anali mafuko a Aseri. Onse amene anawerengedwa analipo 53,400. |
4541 | NUM 26:50 | Awa ndiwo anali mafuko a Nafutali. Onse amene anawerengedwa analipo 45,400. |
4542 | NUM 26:51 | Chiwerengero chonse cha amuna mu Israeli chinalipo 601,730. |
4553 | NUM 26:62 | Alevi onse aamuna a mwezi umodzi kapena kuposera pamenepa analipo 23,000. Iwowo sanawerengedwe pamodzi ndi Aisraeli ena chifukwa sanalandire cholowa pakati pawo. |
4701 | NUM 31:35 | ndi atsikana omwe sanagonepo ndi mwamuna 32,000. |
4712 | NUM 31:46 | anthu 16,000. |
5982 | JOS 7:4 | Choncho kunapita anthu 3,000. Koma iwo anathamangitsidwa ndi anthu a ku Ai. |
6029 | JOS 8:25 | Chiwerengero cha anthu onse a ku Ai, amuna ndi akazi, amene anaphedwa pa tsiku limeneli chinali 12,000. |
6599 | JDG 3:29 | Nthawi imeneyo anapha Amowabu pafupifupi 10,000. Ophedwawo anali anthu amphamvu komanso odziwa kumenya nkhondo, ndipo panalibe ndi mmodzi yemwe anathawa. |
6699 | JDG 7:3 | Tsono lengeza kwa anthu kuti, ‘Aliyense amene akuchita mantha ndi kunjenjemera abwerere kwawo, ndipo achoke kuno ku phiri la Giliyadi.’ ” Choncho anthu 22,000 anachoka, ndipo anatsalira anthu 10,000. |
6731 | JDG 8:10 | Nthawi iyi nʼkuti Zeba ndi Zalimuna ali ku Karikori ndi ankhondo pafupifupi 15,000. Amenewa ndiwo anatsalako mwa ankhondo a anthu akummawa; pakuti anafa ankhondo 120,000. |
6877 | JDG 12:6 | Ndiye amamuwuza kuti, “Nena kuti ‘Shiboleti.’ ” Tsono munthuyo akanena kuti Siboleti popeza samatha kutchula bwino mawuwa, ankamugwira ndi kumupha pomwepo pa madooko a mtsinje wa Yorodani. Nthawi imeneyo anaphedwa Aefereimu 42,000. |
6946 | JDG 15:15 | Anapeza chibwano cha bulu amene anali atangofa kumene. Anachitola ndi kuphera nacho anthu 1,000. |
6984 | JDG 17:2 | “Ndinamva inu mukutemberera munthu amene anaba ndalama zanu zasiliva 1,100. Ndalamazo zili ndi ine, ndinatenga ndine.” Pamenepo amayi akewo anati, “Yehova akudalitse mwana wanga!” |
7081 | JDG 20:25 | Pa tsiku lachiwiri lomwelo Abenjamini anatulukanso mu mzinda wa Gibeya ndipo anaphanso ankhondo 18,000. Onse amene anawaphawo anali odziwa kugwiritsa ntchito bwino malupanga. |
7101 | JDG 20:45 | Koma ena anatembenuka nathawira ku chipululu ku thanthwe la Rimoni. Mwa iwowa Aisraeli anapha Abenjamini 5,000 mʼmisewu yayikulu. Anawapitikitsabe Abenjaminiwo mpaka kufika ku Gidomu ndi kuphanso ena 2,000. |
7455 | 1SA 11:8 | Pamenepo Sauli anawasonkhanitsa ku Bezeki nawawerenga, ndipo Aisraeli analipo 300,000, Ayuda analipo 30,000. |
7489 | 1SA 13:2 | Nthawi ina Sauli anasankha Aisraeli 3,000. Mwa iwowa, 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi ndi ku dziko la mapiri ku Beteli, ndipo 1,000 anali ndi Yonatani ku Gibeya ku Benjamini. Anthu ena onse otsala anawabweza kwawo. |
7691 | 1SA 18:13 | Kotero Sauli anamuchotsa Davide pamaso pake ndi kumuyika kukhala mtsogoleri wa ankhondo 1,000. Choncho Davide ankapita ndi kubwera akutsogolera ankhondowa. |
7866 | 1SA 25:2 | Kunali munthu wina wolemera kwambiri ku Maoni amene malo ake a ntchito anali ku Karimeli. Iyeyu anali ndi mbuzi 1,000 ndi nkhosa 3,000. |
8216 | 2SA 8:4 | Davide analanda magaleta 1,000, anthu 7,000 okwera magaleta pamodzi ndi asilikali oyenda pansi 20,000. Iye anadula mitsempha ya akavalo onse okoka magaleta, koma anasiyapo akavalo 100 okha. |
8217 | 2SA 8:5 | Aramu wa ku Damasiko atabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba, Davide anakantha asilikali 22,000. |
8261 | 2SA 10:18 | Koma iwo anathawa pamaso pa Aisraeli, ndipo Davide anapha anthu okwera pa magaleta 700 ndi ankhondo oyenda pansi 40,000. Davide anaphanso Sobaki mtsogoleri wawo wankhondo ndipo anafera pomwepo. |
8484 | 2SA 18:3 | Koma anthuwo anati, “Inu musapite nafe. Ngati tidzathamangitsidwa, iwowo sadzasamala za ife. Ngakhale theka la ife litafa, iwo sadzasamalako. Koma inuyo ndinu ofunika kuposa asilikali 10,000. Nʼkwabwino kwambiri kuti inu muzititumizira chithandizo kuchokera ku mzindako.” |
8485 | 2SA 18:4 | Mfumu inayankha kuti, “Ine ndichita chimene chili chokukomerani.” Kotero mfumu inayima pambali pa chipata pamene ankhondo onse amayenda mʼmagulu a anthu 100 ndi a 1,000. |
8488 | 2SA 18:7 | Aisraeli anagonjetsedwa kumeneko ndi ankhondo a Davide. Tsiku limenelo anaphedwa anthu okwanira 20,000. |
8704 | 2SA 24:9 | Yowabu anapereka chiwerengero cha anthu ankhondo kwa mfumu: Mu Israeli munali anthu 800,000 amphamvu amene amadziwa kugwiritsa ntchito lupanga ndipo mu Yuda munali anthu 500,000. |
8879 | 1KI 5:12 | Solomoni anapeka miyambi 3,000 ndi kulemba nyimbo 1,005. |
8892 | 1KI 5:25 | ndipo Solomoni anamupatsa Hiramu mitanga ya tirigu 20,000 ngati chakudya cha pa nyumba yake, kuwonjezera pa migolo ya mafuta a olivi yokwana 20,000. Solomoni anapitiriza kupereka zimenezi chaka ndi chaka. |
8894 | 1KI 5:27 | Mfumu Solomoni inasonkhanitsa anthu ogwira ntchito ya thangata mʼdziko lonse la Israeli ndipo anthu athangatawo analipo 30,000. |
8963 | 1KI 7:26 | Mbiyayo inali yonenepa ngati chikhatho ndipo mkombero wake unali ngati mkombero wa chikho, ngati duwa lokongola kwambiri. Mʼmbiyamo munkalowa madzi okwana malita 40,000. |
9051 | 1KI 8:63 | Solomoni anapereka nsembe zachiyanjano kwa Yehova: ngʼombe 22,000, nkhosa ndi mbuzi 120,000. Motero mfumu pamodzi ndi Aisraeli onse anapatula Nyumba ya Yehova. |
9068 | 1KI 9:14 | Koma Hiramu anali atatumiza kwa mfumu golide oposa makilogalamu 4,000. |
9426 | 1KI 20:15 | Choncho Ahabu anawerenga asilikali achinyamata a nduna za mʼzigawo ndipo onse analipo 232. Ndipo anawerenganso ankhondo a ku Israeli ndipo onse analipo 7,000. |
9441 | 1KI 20:30 | Ena onse otsala anathawira ku Afeki, kumene khoma linagwera anthu 27,000. Ndipo Beni-Hadadi anathawira mu mzinda, nakabisala mʼchipinda chamʼkati. |
9882 | 2KI 13:7 | Yehowahazi sanatsale ndi ankhondo ambiri koma 50 okha okwera pa akavalo, magaleta khumi ndi asilikali oyenda pansi 10,000. |
10042 | 2KI 18:14 | Choncho Hezekiya mfumu ya Yuda anatumiza uthenga kwa mfumu ya ku Asiriya ku Lakisi wonena kuti, “Ine ndalakwa. Chokani kuno ndipo ndidzakupatsani chilichonse chimene munene.” Mfumu ya ku Asiriya inalamula mfumu Hezekiya, mfumu ya Yuda, kuti azipereka makilogalamu a siliva okwana 3,000 ndi makilogalamu a golide 1,000. |
10100 | 2KI 19:35 | Usiku umenewo mngelo wa Yehova anapita ku misasa ya ku Asiriya ndi kupha ankhondo 185,000. Ndipo pamene anthu anadzuka mmawa, taonani, mitembo inali ngundangunda! |
10220 | 2KI 24:14 | Anatenga anthu onse a mu Yerusalemu kupita nawo ku ukapolo. Akuluakulu onse pamodzi ndi anthu ankhondo, anthu onse aluso ndi amisiri osula onse pamodzi analipo 10,000. Osauka okha ndiye anatsala mʼdzikomo. |
10222 | 2KI 24:16 | Mfumu ya Babuloni inatumizanso ku Babuloni anthu ankhondo 70,000, anthu amphamvu ndi okonzeka kupita ku nkhondo, anthu aluso ndi amisiri osula 1,000. |
10453 | 1CH 5:21 | Choncho iwo analanda ziweto za Ahagiri: ngamira 50,000, nkhosa ndi mbuzi 250,000 ndi abulu 2,000. Ndiponso anagwira akapolo 100,000, |
10541 | 1CH 7:2 | Ana a Tola ndi awa: Uzi, Refaya, Yerieli, Yahimai, Ibisamu ndi Samueli. Awa anali atsogoleri a mabanja awo. Pa nthawi ya ulamuliro wa Davide zidzukulu za Tola zomwe zinali anthu odziwa kumenya nkhondo zinalipo 22,600. |
10579 | 1CH 7:40 | Onsewa anali zidzukulu za Aseri, atsogoleri a mabanja, anthu omveka, ankhondo olimba mtima, ndi akuluakulu pakati pa atsogoleri anzawo. Chiwerengero cha anthu odziwa kumenya nkhondo chomwe chinalembedwa chinali 26,000. |
10632 | 1CH 9:13 | Ansembe amene anali atsogoleri a mabanja awo analipo 1,760. Anali anthu amphamvu ndi odziwa kutumikira mʼnyumba ya Mulungu. |
10739 | 1CH 12:15 | Anthu a fuko la Gadi amenewa anali atsogoleri; angʼonoangʼono amalamulira anthu 100 pamene akuluakulu amalamulira anthu 1,000. |
10758 | 1CH 12:34 | Anthu a fuko la Zebuloni, analipo 5,000. Iwowa anali asilikali odziwa bwino nkhondo, okhala ndi zida za mtundu uliwonse, okonzekera kudzathandiza Davide ndi mtima umodzi. |
10760 | 1CH 12:36 | Anthu a fuko la Dani, okonzekera nkhondo analipo 28,600. |
10762 | 1CH 12:38 | Ndipo kuchokera kummawa kwa Yorodani, anthu a fuko la Rubeni, Gadi ndi theka la fuko la Manase, amene anali ndi zida za mtundu uliwonse analipo 120,000. |
10899 | 1CH 18:4 | Davide analanda magaleta 1,000, anthu okwera magaleta 7,000 pamodzi ndi asilikali oyenda pansi 20,000. Iye anadula mitsempha ya akavalo onse okoka magaleta, koma anasiyapo akavalo 100 okha. |
10900 | 1CH 18:5 | Aramu wa ku Damasiko atabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya ku Zoba, Davide anakantha asilikali 22,000. |
10930 | 1CH 19:18 | Koma iwo anathawa pamaso pa Aisraeli, ndipo Davide anapha anthu okwera pa magaleta 7,000 ndi ankhondo oyenda pansi 40,000. Iye anaphanso Sofaki, mtsogoleri wawo wankhondo. |
10953 | 1CH 21:14 | Choncho Yehova anabweretsa mliri pa Aisraeli, ndipo unapha Aisraeli 70,000. |
10991 | 1CH 23:3 | Anawerenga Alevi kuyambira a zaka makumi atatu ndi kupitirirapo, ndipo chiwerengero cha amuna onse chinali 38,000. |
11112 | 1CH 26:30 | Kuchokera ku banja la Ahebroni: Hasabiya ndi abale ake, anthu anzeru 1,700. Iwo ankayangʼanira ntchito zonse za Yehova ndi ntchito yonse ya mfumu cha kumadzulo kwa Yorodani. |