Wildebeest analysis examples for:   nya-nya   Word.”)    February 11, 2023 at 19:19    Script wb_pprint_html.py   by Ulf Hermjakob

23001  ZEC 4:10  “Ndani wanyoza tsiku la zinthu zazingʼono? Anthu adzasangalala akadzaona chingwe choyezera mʼmanja mwa Zerubabeli. (“Nyale zisanu ndi ziwirizi ndi maso a Yehova, amene amayangʼanayangʼana pa dziko lapansi.”)