4703 | NUM 31:37 | mwa zimenezi gawo la Yehova linali 675; |
4704 | NUM 31:38 | ngʼombe zinalipo 36,000 ndipo gawo la Yehova linali 72; |
4705 | NUM 31:39 | abulu analipo 30,500 ndipo gawo la Yehova linali 61; |
10802 | 1CH 15:6 | Kuchokera ku banja la Merari, mtsogoleri Asaya ndi abale ake 220; |
10803 | 1CH 15:7 | kuchokera ku banja la Geresomu, mtsogoleri Yoweli ndi abale ake 130; |
10804 | 1CH 15:8 | kuchokera ku banja la Elizafani, mtsogoleri Semaya ndi abale ake 200; |
10805 | 1CH 15:9 | kuchokera ku banja la Hebroni, mtsogoleri Elieli ndi abale ake 80; |
12209 | EZR 8:3 | mwana wa Sekaniya wa fuko la Davide; Zekariya wa fuko la Parosi. Pamodzi ndi iyeyu panalembedwa anthu ena 150; |
20368 | JER 52:23 | Mʼmbali mwake munali makangadza 96; makangadza onse pamodzi analipo 100 kuzungulira ukonde onse. |