Wildebeest analysis examples for: nya-nya “Word?”
February 11, 2023 at 19:19
Script wb_pprint_html.py by Ulf Hermjakob
555
GEN 22:7
Isake anati kwa abambo ake Abrahamu,
“Abambo?”
Abrahamu anayankha, “Ee mwana wanga.” Isake anafunsa, “Moto ndi nkhuni zilipo, koma nanga mwana wankhosa wa nsembe yopsereza ali kuti?”